2 Samueli 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Likasa la Yehova linakhala kunyumba ya Obedi-edomu wa ku Gati kwa miyezi itatu, ndipo Yehova ankadalitsa Obedi-edomu ndi banja lake lonse.+
11 Likasa la Yehova linakhala kunyumba ya Obedi-edomu wa ku Gati kwa miyezi itatu, ndipo Yehova ankadalitsa Obedi-edomu ndi banja lake lonse.+