12 Mfumu Davide inauzidwa kuti: “Yehova wadalitsa nyumba ya Obedi-edomu ndi zinthu zake zonse chifukwa cha Likasa la Mulungu woona.” Choncho Davide anapita kukatenga Likasa la Mulungu woona kunyumba kwa Obedi-edomu nʼkupita nalo ku Mzinda wa Davide, akusangalala.+