2 Samueli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu amene ananyamula+ Likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, Davide anapereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.
13 Anthu amene ananyamula+ Likasa la Yehova atangoyenda mapazi 6, Davide anapereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi chiweto chonenepa.