2 Samueli 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli ankayenda ndi Likasa+ la Yehova akufuula mokondwera+ ndiponso akuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+
15 Davide ndi anthu onse a nyumba ya Isiraeli ankayenda ndi Likasa+ la Yehova akufuula mokondwera+ ndiponso akuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+