-
2 Samueli 6:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Komanso anapatsa anthu onse mikate yozungulira yoboola pakati, makeke a zipatso za kanjedza ndi makeke a mphesa. Anapereka zimenezi ku gulu lonse la Isiraeli, mwamuna ndiponso mkazi. Kenako aliyense anapita kunyumba kwake.
-