2 Samueli 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Mikala mwana wamkazi wa Sauli+ sanakhalepo ndi mwana mpaka tsiku limene anafa.