2 Samueli 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi yonse imene ndinkayenda ndi Aisiraeli,* kodi ndinayamba ndafunsapo atsogoleri a mafuko a Isiraeli amene ndinawasankha kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani simunandimangire nyumba ya mitengo ya mkungudza?’”’
7 Pa nthawi yonse imene ndinkayenda ndi Aisiraeli,* kodi ndinayamba ndafunsapo atsogoleri a mafuko a Isiraeli amene ndinawasankha kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani simunandimangire nyumba ya mitengo ya mkungudza?’”’