2 Samueli 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 pa nthawi imene ndinasankha oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzachititsa kuti uzikhala mwamtendere osavutitsidwa ndi adani ako.+ Komanso Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira nyumba.*+
11 pa nthawi imene ndinasankha oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzachititsa kuti uzikhala mwamtendere osavutitsidwa ndi adani ako.+ Komanso Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira nyumba.*+