2 Samueli 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo chikondi changa chokhulupirika sichidzachoka pa iye ngati mmene ndinachichotsera pa Sauli,+ amene ndinamʼchotsa pamaso pako.
15 Ndipo chikondi changa chokhulupirika sichidzachoka pa iye ngati mmene ndinachichotsera pa Sauli,+ amene ndinamʼchotsa pamaso pako.