2 Samueli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Davide anakhala pansi pamaso pa Yehova ndipo anati: “Ndine ndani ine, Yehova Ambuye Wamkulu Koposa? Ndipo banja lathu* nʼchiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano?+
18 Kenako Mfumu Davide anakhala pansi pamaso pa Yehova ndipo anati: “Ndine ndani ine, Yehova Ambuye Wamkulu Koposa? Ndipo banja lathu* nʼchiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano?+