2 Samueli 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, kuwonjezeranso pamenepa, mwanena kuti nyumba ya mtumiki wanu idzakhazikika mpaka mʼtsogolo kwambiri. Amenewa ndi malangizo* amene mwapereka kwa anthu onse, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.
19 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, kuwonjezeranso pamenepa, mwanena kuti nyumba ya mtumiki wanu idzakhazikika mpaka mʼtsogolo kwambiri. Amenewa ndi malangizo* amene mwapereka kwa anthu onse, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.