2 Samueli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nʼchifukwa chake ndinudi wodabwitsa,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Palibe amene angafanane ndi inu+ komanso palibe Mulungu wina koma inu nokha.+ Zonse zimene tamva zikutsimikizira zimenezi.
22 Nʼchifukwa chake ndinudi wodabwitsa,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa. Palibe amene angafanane ndi inu+ komanso palibe Mulungu wina koma inu nokha.+ Zonse zimene tamva zikutsimikizira zimenezi.