2 Samueli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho inu Yehova Mulungu, chitani zimene mwalonjeza zokhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake ndipo muchite zimenezi mpaka kalekale. Muchite mogwirizana ndi zimene mwalonjeza.+
25 Choncho inu Yehova Mulungu, chitani zimene mwalonjeza zokhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake ndipo muchite zimenezi mpaka kalekale. Muchite mogwirizana ndi zimene mwalonjeza.+