2 Samueli 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Dzina lanu likwezeke mpaka kalekale+ kuti anthu anene kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi Mulungu wa Isiraeli,’ ndipo nyumba ya ine mtumiki wanu Davide ikhazikike pamaso panu.+
26 Dzina lanu likwezeke mpaka kalekale+ kuti anthu anene kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi Mulungu wa Isiraeli,’ ndipo nyumba ya ine mtumiki wanu Davide ikhazikike pamaso panu.+