2 Samueli 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, mwandiululira ine mtumiki wanu kuti, ‘Ndidzakumangira nyumba.’*+ Nʼchifukwa chake ine mtumiki wanu ndalimba mtima kupemphera kwa inu pempheroli.
27 Chifukwa inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, mwandiululira ine mtumiki wanu kuti, ‘Ndidzakumangira nyumba.’*+ Nʼchifukwa chake ine mtumiki wanu ndalimba mtima kupemphera kwa inu pempheroli.