2 Samueli 7:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho dalitsani nyumba ya mtumiki wanu kuti ikhazikike pamaso panu mpaka kalekale.+ Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa mwalonjeza ndipo madalitso anu akhale panyumba ya mtumiki wanu mpaka kalekale.”+
29 Choncho dalitsani nyumba ya mtumiki wanu kuti ikhazikike pamaso panu mpaka kalekale.+ Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa mwalonjeza ndipo madalitso anu akhale panyumba ya mtumiki wanu mpaka kalekale.”+