2 Samueli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Davide anagonjetsa Afilisiti+ ndipo anawalanda mzinda wa Metege-ama.