2 Samueli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense amene anatsala mʼnyumba ya Sauli amene ndingamusonyeze chikondi chokhulupirika chifukwa cha Yonatani?”+
9 Kenako Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense amene anatsala mʼnyumba ya Sauli amene ndingamusonyeze chikondi chokhulupirika chifukwa cha Yonatani?”+