2 Samueli 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno panali mtumiki wa nyumba ya Sauli dzina lake Ziba.+ Choncho anaitanidwa kuti apite kwa Davide, ndipo mfumu inamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Ziba?” Iye anayankha kuti: “Inde, ndine mtumiki wanu.”
2 Ndiyeno panali mtumiki wa nyumba ya Sauli dzina lake Ziba.+ Choncho anaitanidwa kuti apite kwa Davide, ndipo mfumu inamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Ziba?” Iye anayankha kuti: “Inde, ndine mtumiki wanu.”