2 Samueli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mfumu inati: “Kodi pali aliyense amene anatsala mʼnyumba ya Sauli amene ndingamusonyeze chikondi chokhulupirika cha Mulungu?” Ziba anauza mfumu kuti: “Alipo mwana wamwamuna wa Yonatani, wolumala mapazi.”+
3 Mfumu inati: “Kodi pali aliyense amene anatsala mʼnyumba ya Sauli amene ndingamusonyeze chikondi chokhulupirika cha Mulungu?” Ziba anauza mfumu kuti: “Alipo mwana wamwamuna wa Yonatani, wolumala mapazi.”+