2 Samueli 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Akukhala kuti?” Ziba anayankha mfumu kuti: “Mʼnyumba ya Makiri,+ mwana wamwamuna wa Amiyeli, ku Lo-debara.”
4 Kenako mfumu inamufunsa kuti: “Akukhala kuti?” Ziba anayankha mfumu kuti: “Mʼnyumba ya Makiri,+ mwana wamwamuna wa Amiyeli, ku Lo-debara.”