-
2 Samueli 9:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mefiboseti mwana wa Yonatani, mwana wa Sauli, atalowa nʼkuona Davide, nthawi yomweyo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi. Kenako Davide anati: “Mefiboseti!” Iye anayankha kuti: “Ine mtumiki wanu.”
-