2 Samueli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndikusonyeza ndithu chikondi chokhulupirika+ chifukwa cha Yonatani bambo ako. Ndikubwezera malo onse a agogo ako a Sauli ndipo iweyo nthawi zonse uzidya patebulo langa.”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Nsanja ya Olonda,5/15/2002, tsa. 19
7 Ndiyeno Davide anamuuza kuti: “Usaope. Ndikusonyeza ndithu chikondi chokhulupirika+ chifukwa cha Yonatani bambo ako. Ndikubwezera malo onse a agogo ako a Sauli ndipo iweyo nthawi zonse uzidya patebulo langa.”+