2 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake kufika pansi ndipo anati: “Ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mundikumbukire, galu wakufa+ ngati ine?”
8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake kufika pansi ndipo anati: “Ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mundikumbukire, galu wakufa+ ngati ine?”