2 Samueli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno mfumu inaitana Ziba, mtumiki wa Sauli, nʼkumuuza kuti: “Chilichonse chimene chinali cha Sauli komanso chimene chinali cha nyumba yake, ndikupereka kwa mdzukulu wa mbuye wako.+
9 Ndiyeno mfumu inaitana Ziba, mtumiki wa Sauli, nʼkumuuza kuti: “Chilichonse chimene chinali cha Sauli komanso chimene chinali cha nyumba yake, ndikupereka kwa mdzukulu wa mbuye wako.+