2 Samueli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mefiboseti anali ndi mwana wamngʼono wamwamuna dzina lake Mika,+ ndipo anthu onse amʼnyumba ya Ziba anali antchito a Mefiboseti.
12 Mefiboseti anali ndi mwana wamngʼono wamwamuna dzina lake Mika,+ ndipo anthu onse amʼnyumba ya Ziba anali antchito a Mefiboseti.