2 Samueli 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mefiboseti ankakhala ku Yerusalemu ndipo ankadya patebulo la mfumu nthawi zonse.+ Iye anali wolumala mapazi.+
13 Choncho Mefiboseti ankakhala ku Yerusalemu ndipo ankadya patebulo la mfumu nthawi zonse.+ Iye anali wolumala mapazi.+