-
2 Samueli 10:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zitatero, Davide anati: “Ndimusonyeza Hanuni mwana wa Nahasi chikondi chokhulupirika ngati mmene bambo ake anandisonyezera chikondi chokhulupirika.” Choncho Davide anatumiza atumiki ake kuti akamutonthoze chifukwa cha imfa ya bambo ake. Koma atumiki a Davidewo atangofika mʼdziko la Aamoni,
-