-
2 Samueli 10:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndiyeno anamuuza kuti: “Ukaona kuti Asiriya akundigonjetsa, ubwere udzandipulumutse. Koma Aamoni akayamba kukugonjetsa, ineyo ndibwera kudzakupulumutsa.
-