2 Samueli 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Asiriya ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli, anasonkhananso pamodzi.+