2 Samueli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu onse amene anali atumiki a Hadadezeri ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli, nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Aisiraeli nʼkuyamba kuwatumikira.+ Asiriya anachita mantha kwambiri moti sanayesenso kuthandiza Aamoni.
19 Mafumu onse amene anali atumiki a Hadadezeri ataona kuti agonjetsedwa ndi Aisiraeli, nthawi yomweyo anakhazikitsa mtendere ndi Aisiraeli nʼkuyamba kuwatumikira.+ Asiriya anachita mantha kwambiri moti sanayesenso kuthandiza Aamoni.