2 Samueli 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumayambiriro kwa chaka, pa nthawi imene mafumu ankapita kukamenya nkhondo, Davide anatumiza Yowabu ndi atumiki ake komanso asilikali onse Aisiraeli kuti akaphe Aamoni ndipo iwo anazungulira mzinda wa Raba.+ Koma Davide anatsala ku Yerusalemu.+
11 Kumayambiriro kwa chaka, pa nthawi imene mafumu ankapita kukamenya nkhondo, Davide anatumiza Yowabu ndi atumiki ake komanso asilikali onse Aisiraeli kuti akaphe Aamoni ndipo iwo anazungulira mzinda wa Raba.+ Koma Davide anatsala ku Yerusalemu.+