2 Samueli 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anatuma anthu kuti akamutenge.+ Choncho mkaziyo anabweradi ndipo Davide anagona naye.+ (Zimenezi zinachitika pa nthawi imene mkaziyo ankadziyeretsa.*)+ Kenako mkaziyo anabwerera kunyumba kwake.
4 Davide anatuma anthu kuti akamutenge.+ Choncho mkaziyo anabweradi ndipo Davide anagona naye.+ (Zimenezi zinachitika pa nthawi imene mkaziyo ankadziyeretsa.*)+ Kenako mkaziyo anabwerera kunyumba kwake.