-
2 Samueli 11:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Uriya anauza Davide kuti: “Likasa+ komanso asilikali a Isiraeli ndi Yuda akukhala mʼmisasa, ndipo mbuyanga Yowabu pamodzi ndi atumiki anu mbuyanga ali mumsasa kutchire. Ndiye ine ndikalowe mʼnyumba yanga kukadya chakudya, kumwa ndi kugona ndi mkazi wanga?+ Ndithu ndikulumbira mʼdzina lanu mfumu muli apa, sindingachite zimenezo!”
-