2 Samueli 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mʼkalatayo analembamo kuti: “Muike Uriya kutsogolo kumene nkhondo yakula, ndipo inu mubwerere mʼmbuyo kuti amuphe.”+
15 Mʼkalatayo analembamo kuti: “Muike Uriya kutsogolo kumene nkhondo yakula, ndipo inu mubwerere mʼmbuyo kuti amuphe.”+