21 Ndi ndani anapha Abimeleki+ mwana wa Yerubeseti+ ku Tebezi? Kodi si mkazi amene anali pamwamba pa mpanda yemwe anaponya mwala wa mphero? Nʼchifukwa chiyani munauyandikira kwambiri mpandawo?’ Iwe ukanene kuti, ‘Nayenso mtumiki wanu Uriya Muhiti, wafa.’”