2 Samueli 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Davide atamva zimenezi anauza munthuyo kuti: “Ukamuuze Yowabu kuti, ‘Usade nkhawa ndi zimenezi, aliyense akhoza kuphedwa ndi lupanga. Inuyo menyanani ndi anthu amumzindawo mwamphamvu ndipo muwagonjetse.’+ Komanso ukamulimbikitse.”
25 Davide atamva zimenezi anauza munthuyo kuti: “Ukamuuze Yowabu kuti, ‘Usade nkhawa ndi zimenezi, aliyense akhoza kuphedwa ndi lupanga. Inuyo menyanani ndi anthu amumzindawo mwamphamvu ndipo muwagonjetse.’+ Komanso ukamulimbikitse.”