2 Samueli 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nthawi yolira maliro itatha, Davide anatumiza anthu kuti akatenge Bati-seba nʼkubwera naye kunyumba kwake kuti akhale mkazi wake+ ndipo anamuberekera mwana wamwamuna. Koma zimene Davide anachitazi zinamunyansa kwambiri Yehova.+
27 Nthawi yolira maliro itatha, Davide anatumiza anthu kuti akatenge Bati-seba nʼkubwera naye kunyumba kwake kuti akhale mkazi wake+ ndipo anamuberekera mwana wamwamuna. Koma zimene Davide anachitazi zinamunyansa kwambiri Yehova.+