2 Samueli 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Atafika+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene ankakhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Nsanja ya Olonda,5/1/2010, tsa. 30
12 Yehova anatuma Natani+ kwa Davide. Atafika+ anamuuza kuti: “Panali amuna awiri amene ankakhala mumzinda umodzi. Wina anali wolemera ndipo wina anali wosauka.