2 Samueli 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako+ ndiponso ndinaika akazi a mbuye wako+ mʼmanja mwako. Ndinakupatsanso nyumba ya Isiraeli ndi ya Yuda.+ Zinthu zimenezi zikanakhala kuti sizinakukwanire, ndinali wokonzeka kukuwonjezeranso zina.+
8 Ndinakupatsa nyumba ya mbuye wako+ ndiponso ndinaika akazi a mbuye wako+ mʼmanja mwako. Ndinakupatsanso nyumba ya Isiraeli ndi ya Yuda.+ Zinthu zimenezi zikanakhala kuti sizinakukwanire, ndinali wokonzeka kukuwonjezeranso zina.+