2 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wanena kuti, ‘Ndikugwetsera tsoka kuchokera mʼnyumba yako+ yomwe komanso iwe ukuona. Ndidzatenga akazi ako nʼkuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi akowo masanasana.+
11 Yehova wanena kuti, ‘Ndikugwetsera tsoka kuchokera mʼnyumba yako+ yomwe komanso iwe ukuona. Ndidzatenga akazi ako nʼkuwapereka kwa mwamuna wina,+ ndipo iye adzagona ndi akazi akowo masanasana.+