2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero, Davide anauza Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
13 Zitatero, Davide anauza Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+