2 Samueli 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero Davide anachonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya. Davide akalowa mʼnyumba usiku ankagona pansi.+
16 Zitatero Davide anachonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya. Davide akalowa mʼnyumba usiku ankagona pansi.+