2 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anayankha kuti: “Mwanayo ali ndi moyo, ndimasala kudya+ ndipo ndimalira chifukwa ndimaganiza kuti, ‘Angadziwe ndani? Mwina Yehova angandichitire chifundo ndipo angalole kuti mwanayu akhale ndi moyo.’+
22 Iye anayankha kuti: “Mwanayo ali ndi moyo, ndimasala kudya+ ndipo ndimalira chifukwa ndimaganiza kuti, ‘Angadziwe ndani? Mwina Yehova angandichitire chifundo ndipo angalole kuti mwanayu akhale ndi moyo.’+