2 Samueli 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiye poti wamwalira, ndisalenso kudya chifukwa chiyani? Kodi ndingamuukitse?+ Inenso tsiku lina ndidzamwalira,+ koma iyeyo sangabwerere kwa ine.”+
23 Ndiye poti wamwalira, ndisalenso kudya chifukwa chiyani? Kodi ndingamuukitse?+ Inenso tsiku lina ndidzamwalira,+ koma iyeyo sangabwerere kwa ine.”+