-
2 Samueli 12:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Tsopano sonkhanitsani asilikali amene atsala kuti mumenyane ndi anthu amumzindawu nʼkuulanda, chifukwa mukapanda kutero ndiulanda ndine, ndipo dzina langa ndi limene litchuke.”
-