-
2 Samueli 13:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zimenezi zinamuvutitsa maganizo kwambiri Aminoni, moti anadwala chifukwa cha mchemwali wake Tamara. Popeza Tamara anali namwali, zinkaoneka kuti palibe chimene Aminoni angachite.
-