2 Samueli 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehonadabu anafunsa Aminoni kuti: “Nʼchifukwa chiyani iwe mwana wa mfumu tsiku lililonse ukumaoneka wosasangalala? Tandiuza.” Aminoni anayankha kuti: “Ine ndikumufuna kwambiri Tamara, mchemwali wake+ wa mʼbale wanga Abisalomu.”
4 Ndiyeno Yehonadabu anafunsa Aminoni kuti: “Nʼchifukwa chiyani iwe mwana wa mfumu tsiku lililonse ukumaoneka wosasangalala? Tandiuza.” Aminoni anayankha kuti: “Ine ndikumufuna kwambiri Tamara, mchemwali wake+ wa mʼbale wanga Abisalomu.”