-
2 Samueli 13:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho Aminoni anagona nʼkunamizira kudwala. Zitatero mfumu inabwera kudzamuona ndipo Aminoni anauza mfumuyo kuti: “Ndikupempha kuti mchemwali wanga Tamara abwere kudzandiphikira makeke ine ndikuona kuti ndidye chakudya kuchokera mʼmanja mwake.”
-