2 Samueli 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero, Davide anatumiza uthenga kwa Tamara wakuti: “Chonde, pita kunyumba kwa mchimwene wako Aminoni ukamukonzere chakudya.”*
7 Zitatero, Davide anatumiza uthenga kwa Tamara wakuti: “Chonde, pita kunyumba kwa mchimwene wako Aminoni ukamukonzere chakudya.”*